Pamene Hazrat Bilaal (Radhiya Allaahu ‘anhu) adatsala pang’ono kumwalira, mkazi wake adayamba kunena kuti: “Ha! Ndi zomvetsa chisoni bwanji! Mukuchoka m’dziko lino!” Hazrat Bilaal (Radhiya Allahu anhu) anayankha kuti: “Zili zokondweretsa ndi zosangalatsa kuti mawa tikukakumana ndi abwenzi athu, tikakumana ndi Muhammad (Swalla Allaahu ‘alayhi wa sallam) ndi maswahaba ake.”
Read More »Kuwerenga Durood Pamkumano
عن أنس عن النبي صلى الله عليه وسلم قال: ما من عبدين متحابين في الله يستقبل أحدهما صاحبه فيصافحه ويصليان على النبي صلى الله عليه وسلم إلا لم يفترقا حتى تغفر ذنوبهما ما تقدم منهما وما تأخر (مسند أبي يعلى الموصلي، الرقم: 2960، وفيه درست بن حمزة وهو ضعيف كما …
Read More »Tisadaswali
6. Onetsetsani kuti mukuswali mutavala chisoti mmutu chifukwa idali sunnah ya Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) komanso ma swahabah (radhwiyallahu anhum) kuvala chisoti akamaswali. روي عن ابن عباس رضي الله عنهما أن رسول الله صلى الله عليه وسلم كان يلبس القلانس تحت العمائم ويلبس العمائم بغير القلانس (جمع الوسائل صـ 207)[1] …
Read More »Nsembe ya maswahabah radhwiyallahu anhum pa Mtumiki (swallallahu alaih wasallam)
Nyumba ya Bibi Faatimah (radhiyallahu anha) idali potalikirako ndi nyumba ya Mtumiki (sallallahu alaih wasallam). Tsiku lina Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adamuuza kuti “khumbo langa ndiloti udzikhala nane pafupi” Bibi Faatimah (radhiyallahu anha) adayankha nati, Nyumba ya Haarithah ili pafupi ndi yanu, ngati mungamupemphe kuti tisinthanitse ndi yanga adzavomera mwansangala. …
Read More »Tafseer Ya Surah Quraish
لِإِيلفِ قُرَيْشٍ ﴿١﴾ اِلٰفِهِمْ رِحْلَةَ الشِّتَآءِ وَالصَّيْفِ ﴿٢﴾ فَلْيَعْبُدُوا۟ رَبَّ هٰذَا الْبَيْتِ ﴿٣﴾ الَّذِىٓ أَطْعَمَهُم مِّن جُوْعٍ وَاٰمَنَهُمْ مِّنْ خَوْفِۭ ﴿٤﴾ Chifukwa cha chitetezo cha ma Quraishi, chitetezo chimene amasangalala nacho m’maulendo awo m’miyezi yachisanu ndi m’nyengo yachilimwe. Kotero akuyenera kupembedza Mbuye wa nyumba yopatulika (Ka’aba), yemwe adawapatsa chakudya chothetsa njala yawo ndi chitetezo ku …
Read More »Kuwerenga Duruud ngati waiwala China chake
عن أنس رضي الله عنه قال: قال رسول الله صلى الله عليه وسلم: إذا نسيتم شيئا فصلوا علي تذكروه إن شاء الله تعالى (أخرجه أبو موسى المديني بسند ضعيف كما في القول البديع صـ 448) Sayyiduna Anas (radhwiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) adati: ngati waiwala chinachake udziwerenga …
Read More »Tisadaswali
1. konzekerani za swalah nthawi yabwino ndi kuonetsetsa kuti simunazikonzekeretse thupi lokha koma ndi maganizo omwe mwakonzeka zoti mukukaima pamanso pa Allah.[1] 2. onetsetsani kuti mukupemphera swalah iliyonse munthawi yake komanso mwakaswali pagulu ku mnzikiti.[2] عن أبي هريرة رضي الله عنه قال قال رسول الله صلى الله عليه وسلم لولا …
Read More »Palibe malo mu Chisilamu kwa amene a kunyoza ma Swahaabah (Radhiyallahu anhum)
Tsiku linalake Munthu wina anafika kwa Zainul Aabidiin, Aliy bin Husain rahimahullah ndipo adafunsa: Oh chidzukulu cha Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) maganizo anu ndi otani pa nkhani ya Uthmaan (radhwiyallahu anhu)? Atazindikira za nkwiyo wa munthuyu pa Uthmaan (radhwiyallahu anhu, Olemekeza Zainul Aabidiin (rahimahullah)adamulongosolera munthuyo kuti: Oh m’bale wanga okondeka! …
Read More »Mmene Ma Swahaabah Ankachitira Zokhudza Salaah Yapagulu
Sayyiduna Abdullah bin Masuud (radhwiyallahu anhu) zikunenedwa kuti iye adati: “Sungani Swalah zanu zisanu pa tsiku popemphera pa malo amene adhaan yaitanidwa (monga musjid). Ndithu, Swalah izi (Fardh) m’Musjid ndi zochokera ku Sunan huda (mapembedzedwe olamuridwa mu Deen). Allah wamulamula Nabiy wake sunan huda (mapembedzedwe amenewa ndi chiongoko kwa inu). …
Read More »Mphavu za Aliyy (radhiyallahu anhu) pa nkhondo ya Uhud
Pa nkhondo ya Uhud ma swahabah (radhwiyallahu anhum) adagonjetsedwa kwambiri ndi adani ndipo ambiri adaphedwa kumene, Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) Adazunguliridwa ndi adani ndikuvulazidwa kwambiri, nthawi imeneyi mphekesera idayamba kumveka kuti Mtumiki waphedwa, maswahabah atamva mphekesera imeneyi adasweka mitima ndikutaya chiyembekezo. Hazrat Ali (radhwiyallahu anhu) akufotokoza kuti: tidazunguliridwa ndi adani …
Read More »