Tafseer Ya Surah Lahab

بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ تَبَّتْ يَدَا أَبِي لَهَبٍ وَتَبَّ ‎﴿١﴾‏ مَا أَغْنَىٰ عَنْهُ مَالُهُ وَمَا كَسَبَ ‎﴿٢﴾‏ سَيَصْلَىٰ نَارًا ذَاتَ لَهَبٍ ‎﴿٣﴾‏ وَامْرَأَتُهُ حَمَّالَةَ الْحَطَبِ ‎﴿٤﴾‏ فِي جِيدِهَا حَبْلٌ مِّن مَّسَدٍ ‎﴿٥﴾ Manja awiri a Abu Lahab awonongeke, ndipo awonongekeretu! chuma chake sichidampindulire ngakhalenso zomwe adapeza. Posachedwapa adzalowa m’moto wodzadza ndi malawi oyaka, komanso mkazi wake, woipa wonyamula nkhuni …

Read More »

Hazrat Umar (radhwiyallahu ‘anhu) Kulemekeza Azwaaj-e-Mutahharaat (radhwiyallahu ‘anhunna)

Olemekezeka Aslam (rahimahullah), kapolo wa Sayyiduna Umar (radhwiyallahu anhu), akufotokoza kuti Umar (radhwiyallahu ‘anhu) anali ndi mbale zisanu ndi zinayi zomwe zidasungidwa kuti azitumizira mphatso kwa Azwaa-e-Mutwahharaat (akazi olemekezeka a Mtumiki (Swallallaahu ‘alayhi wasallam) di amayi a Ummah). Olemekezeka Aslam (rahimahuliah) adanena kuti nthawi iliyonse kukafika chakudya chokoma, zipatso kapena …

Read More »

Kapempheredwe ka Azimayi

Mazhab anayi Kuyambira nthawi ya Sayyiduna Rasulullah, ma Swahaabah, Taabi’een ndi zaka mazana zotsatira, akazi ankalamulidwa kuswali m’njira yosiyana ndi Swalaah ya amuna m’magawo ena za swalah. Madhabu onse anayi (omwe ndi Hanafi, Maliki, Shafi’i ndi Hambali) onse amagwirizana pa mfundo yakuti Swalaah ya akazi imasiyana ndi Swalaah ya amuna …

Read More »

Kusamalitsa pa Chuma cha Anthu

Kusamalitsa komwe olemekezeka Umar (radhwiyallahu ‘anhu)adachita pa kagwiritsidwe ntchito ka chuma cha anthu kunalidi kosasimbika. Nthawi ina, musk (mtundu wa mafuta onunkhira) anabweretsedwa kuchokera ku Bahrain. Ngati chuma cha anthu onse, Umar (radhwiya allaahu ‘anhu) adati: “Ndikulumbirira kwa Allah! Ndikufuna nditapeza munthu wodziwa kuyeza zinthu kuti andipimire mafutawa kuti ndiwagawe …

Read More »

Kapempheredwe ka Azimayi

Chilichonse cha chipembedzo cha Chisilamu chokhudzana ndi akazi chimakhanzikika pa kukhala odzichepetsa komanso wamanyazi. Pachifukwa ichi ndi pamene Chisilamu chikulamula amayi kuti azikhala m’nyumba zawo, kukhala obisika kwa amuna achilendo, komanso kuti asachoke m’nyumba zawo popanda chifukwa chenicheni pa Sharia. M’mene mkazi walamulidwira kuswali Swalah yake – kuyambira pa chovala …

Read More »

Olemekezeka Umar (radhwiyallahu ‘anhu) adzikumbutsa za Kuyankha mafunso pa Tsiku Lachiweruzo

Ngakhale Allah Ta’ala adamudalitsa Umar (radhwiyallahu ‘anhu) pokhala m’gulu la anthu khumi omwe adalonjezedwa kukalowa ku Jannah ali padziko lino lapansi, ndipo ngakhale adali khalifah wachiwiri wa Chisilamu, adali wodzichepetsa kwambiri ndikuwopa kuyankha mafunso pamaso pa Allah Ta’ala pa tsiku la Qiyaamah. Zikunenedwa kuti nthawi ina, Olemekezeka Umar (radhwiyallahu ‘anhu) …

Read More »

Kumudziwa Allah

Allah ndiye Mlengi ndi Mdyetsi wa zolengedwa zonse. Cholengedwa Chilichonse , ngakhale milalang’amba, dzuŵa, nyenyezi, mapulaneti, kapena nthaka ndi zonse zili m’menemo, ndi zolengedwa za Allah. Munthu amene amasinkhasinkha ndi kusakasaka za ukulu ndi kukongola kwa zolengedwa zonsezi angalingalire bwino lomwe ukulu ndi kukongola kwa Amene adazilenga! Allah akutiitanira m’Qur’an …

Read More »

Qa’dah ndi Salaam

9. Osatsitsa kapena kugwedeza mutu pamene mukupanga salaamu. 10. Tembenuzirani nkhope yanu mbali zonse ziwiri moti amene ali m’mbuyo mwanu athe kuona tsaya lanu.[1] 11. Werengani mawu oti اَسْتَغْفِرُ الله katatu pambuyo pa salaam.[2] 12. Pangani ma dua popeza iyi ndi nthawi yoyankhidwa ma dua.[2] 13. Werengani Tasbeeh Faatimi kutha …

Read More »

Hazrat Ali (radhwiyallaahu ‘anhu) Akufuna Kukumana ndi Allah Ta’ala ndi zochita za Hazrat Umar (radhwiyallaahu ‘anhu)

Olemekezeka Abdullah bin Abbaas (radhwiyallaahu ‘anhuma) akunena kuti: Ndinalipo pa nthawi yomwe mtembo wa Umar (radhwiyallahu ‘anhu) unkaikidwa pa Jeneza ataphedwa. Anthu anayamba kuthamangira pamene padali thupi lake. Pamene ankayembekezera kuti mtembo wake utulutsidwe ndi kuikidwa m’manda, iwo ankawerenga durood kumfunira zabwino Rasulullah (swallallaahu ‘alayhi wasallam) ndikumamupemphera Umar (radhwiyallahu ‘anhu). …

Read More »

Qa’dah ndi Salaam

5. Ngati ukuswali rakaah zitatu kapena zinayi kenako ukamaliza kuwerenga tashahhud m’qa’dah yoyamba, nawenso werenga swalaah alan Nabi (durood). Powerenga Swala ya alan Nabi (durood), اللهم صل على محمد  werengani mpaka dzina lodalitsika la Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) Kenako imirirani rakaah yachitatu. Musapange dua pambuyo powerenga Swalaat alan Nabi (durood).[1] …

Read More »