11. Musayankhule pamene mukupanga Adhaan.[1] 12. Musasokoneze mawu Adhaan kapena kupanga kusintha mawu mmatchuridwe.[2] عن يحيى البكاء قال قال رجل لابن عمر رضي الله عنهما إني لأحبك في الله فقال ابن عمر رضي الله عنهما لكني أبغضك في الله قال ولم قال إنك تتغنى في أذانك وتأخذ عليه أجرا (مجمع …
Read More »Tafseer Ya Surah Takaathur
اَلْهٰكُمُ التَّكَاثُرُ ﴿١﴾ حَتّٰى زُرْتُمُ الْمَقَابِرَ ﴿٢﴾ كَلَّا سَوْفَ تَعْلَمُوْنَ ﴿٣﴾ ثُمَّ كَلَّا سَوْفَ تَعْلَمُوْنَ ﴿٤﴾ كَلَّا لَوْ تَعْلَمُوْنَ عِلْمَ الْيَقِينِ ﴿٥﴾ لَتَرَوُنَّ ٱلْجَحِيمَ ﴿٦﴾ ثُمَّ لَتَرَوُنَّهَا عَيْنَ ٱلْيَقِينِ ﴿٧﴾ ثُمَّ لَتُسْـَٔلُنَّ يَوْمَئِذٍ عَنِ ٱلنَّعِيمِ ﴿٨﴾ Kwakutangwanitsani kusonkhanitsa (chuma chambiri ndi ana). Mpakana mwapita kumanda (mwamwalira ndikuikidwa m’manda). Sichincho, mudziwa …
Read More »Kupeza Chifundo Chochuluka Cha Allah Ta’ala
عن ابن عمر وأبي هريرة رضي الله عنهما قالا قال رسول الله صلى الله عليه وسلم صلوا علي صلى الله عليكم (الكامل لابن عدي، الرقم: ١١٠٨٦، وإسناده ضعيف كما في التيسير للمناوي ٢/٩٣) Sayyiduna Abdullah bin Umar komanso Abu Hurairah (radhwiyallahu anhuma) akusimba kuti, Nabi (sallallahu alaih wasallam) adati, ndifunireni …
Read More »Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana
9. Lowetsani zala zanu za nkomba phala m’makutu mwanu pamene mukupanga Adhaan.
Sayyiduna Sa’d Al-Qurazi (radhiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adamuuza Bilaal (radhiyallahu anhu) kuti alowetse zala zake m’makutu mwake (pamene ankapanga Adhaan) ndip adati “izi zizikuthandiza kuti udzikweza mawu kwambiri popanga Adhaan.”
Read More »Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana
6. Yang’anani ku Qiblah pamene mukupanga Adhaan.[1] عن معاذ بن جبل رضي الله عنه قال … فجاء عبد الله بن زيد رجل من الأنصار وقال فيه فاستقبل القبلة … (سنن أبي داود، الرقم: 507)[2] Sayyiduna Mu’adh bin Jabal (radhiyallahu anhu) akusimba kuti, “…Sayyiduna Abdullah bin Zaid (radhiyallahu anhu) amene adali …
Read More »Chiyambi Chakuwala Kwa Munthu Patsiku Lachiweruzo
عن ابن عمر رضي الله عنهما قال قال رسول الله صلى الله عليه وسلم زينوا مجالسكم بالصلاة علي فإن صلاتكم علي نور لكم يوم القيامة (الفردوس بمأثور الخطاب، الرقم: ٣٣٣٠، وإسناده ضعيف كما في القول البديع صـ 278) Sayyiduna Ibnu Umar (radhiyallahu anhu) akusimba kuti, Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adati …
Read More »Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana
4. Kupanga Adhaana ndimau okweza kwambiri.
Sayyiduna Abdullah mwana wa Zaydu (radhiyallah anhu) akusimba kuti ...... Kenako ndinamuuuza Mtumiki (sallallah alayhi wasallam zamaloto amene ndidalota (komanso kapangidwe ka adhaana kamene ndinaphunzitsidwira mmalotomo).Mtumiki (sallallah alayhi wasallam) adayankha nati; Ndithudi ndimaloto owona inshaa Allah, Pita kwa Bilaal radhiyallah anhu ukamphunzitse mawu aadhaana amene wamva mmaloto ako kuti naye adzipanga adhaana pogwiritsa ntchito mawu amenewa, Chifukwa choti Bilaliyo mawu ake ndiokwera kwambiri kuposa mawu ako.
Read More »Chizindikiro chokhala ndi makhalidwe oipa komanso kusayamika
عن قتادة رحمه الله قال: قال رسول الله صلى الله عليه وسلم: من الجفاء أن أذكر عند الرجل فلا يصلي علي (الإعلام بفضل الصلاة على النبي صلى الله عليه وسلم للنميري، الرقم: ٢٠٩، ورواته ثقات كما في القول البديع صـ ٣١١) Sayyiduna Qataadah (rahimahullah) akufotokoza kuti Mtumiki (sallallahua alaih wasallam) …
Read More »Njira Ya Sunnah Yopangira Adhaana
1. Onetsetsani kuti chitsimikizo chanu chopangira adhaana chikhale kusangalatsa Allah Taala basi. عن ابن عباس رضي الله عنهما أن النبي صلى الله عليه وسلم قال من أذن سبع سنين محتسبا كتبت له براءة من النار (سنن الترمذي، الرقم: 206)[1] Sayyiduna Ibn Abbas Allah asangalare naye akunena kuti; Bwana wathu Mtumiki …
Read More »Kusiya ntchito yomwe ingakakulowetse ku Jannah
Sayyiduna Husain bin Aliy (radhiyallahu anhuma) akufotokoza kuti Mthenga wa Allah madalitso ndi ntendere zipite kwa iye adati: munthu amene dzina langa latchulidwa pamaso pake ndiye osandifunira zabwino (osawerenga Durood) munthu ameneyo wasiya ntchito yabwino yokakulowetsa ku Jannah.
Read More »